1 Chronicles 7:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo kulembedwa kwao potsata kubadwa kwao ndiponso malinga ndi mibadwo yao, pokhala atsogoleri a mabanja a makolo ao, analipo 20,200, ankhondo amphamvu okhaokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayesedwa mwa chibadwidwe chao, mwa mibadwo yao, akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi makumi awiri mphambu mazana awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa mndandanda wa mʼbado wawo panali atsogoleri a mabanja ndi anthu 20,200 odziwa kumenya nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayesedwa mwa cibadwidwe cao, mwa mibadwo yao, akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi makumi awiri mphambu mazana awiri.