1 Chronicles 8:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Benjamini adabereka Bela mwana wake wachisamba, Asibele mwana wake wachiŵiri, Ahara mwana wake wachitatu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Benjamini anabala Bela mwana wake woyamba, Asibele wachiwiri, ndi Ahara wachitatu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Benjamini anabereka Bela mwana wake woyamba, wachiwiri Asibeli, wachitatu Ahara,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Benjamini anabala Bela mwana wace vyoyamba, Asibeli waciwiri, ndi Ahara wacitatu,