1 Chronicles 8:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Elipaala naŵa: Ebere, Misamu ndi Semedi. Semedi ndiye adamanga mizinda ya Ono ndi Lodi pamodzi ndi midzi yake yomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Elipaala: Eberi, ndi Misamu, ndi Semedi, amene anamanga Ono, ndi Lodi ndi milaga yake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Elipaala anali awa: Eberi, Misamu, Semedi (amene anamanga mizinda ya Ono ndi Lodi ndi midzi yake yozungulira)
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Elipaala: Eberi, ndi Misamu, ndi Semedi, amene anamanga Ono, ndi Ludi ndi miraga yace,