1 Chronicles 8:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Beriya ndi Sema anali atsogoleri a mabanja okhala ku mzinda wa Aiyaloni. Iwowo adathaŵitsa nzika za ku Gati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Beriya, ndi Sema; ndiwo akulu a nyumba za makolo a iwo okhala m'Ayaloni, amene anathawitsa okhala m'Gati;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso Beriya ndi Sema, amene anali atsogoleri a mabanja a amene ankakhala ku Ayaloni ndipo anathamangitsa nzika za ku Gati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Beriya, ndi Sema; ndiwo akuru a nyumba za makolo a iwo okhala m'Ayaloni, amene anathawitsa okhala m'Gati;