1 Chronicles 8:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaya, Beraya ndi Simiratu anali zidzukulu za Simei.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Adaya, ndi Beraya, ndi Simiratu, ana a Simei;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adaya, Beraya ndi Simirati anali ana a Simei.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Adaya, ndi Beraya, ndi Simirati, ana a Simei;