1 Chronicles 8:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yeiyele, amene adaamanga Gibiyoni, ankakhala ku Gibiyoni komweko. Mkazi wake anali Maaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'Gibiyoni anakhala atate a Gibiyoni, dzina la mkazi wake ndiye Maaka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeiyeli amene amabereka Gibiyoni ankakhala ku Gibiyoni. Dzina la mkazi wake linali Maaka,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'Gibeoni anakhala atate a Gibeoni, dzina la mkazi wace ndiye Maaka;