1 Chronicles 8:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wake wachisamba anali Abidoni, pambuyo pa iyeyo panali Zuri, Kisi, Baala, Nere, Nadabu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mwana wake woyamba ndiye Abidoni, opondana naye ndi Zuri, ndi Kisi, ndi Baala, ndi Nadabu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo mwana wake woyamba anali Abidoni, motsatana ndi Zuri, Kisi, Baala, Neri, Nadabu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mwana wace woyamba ndiye Abidoni, opondana naye ndi Zuri, ndi Kisi, ndi Baala, ndi Nadabu,