1 Chronicles 8:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nere adabereka Kisi, Kisi adabereka Mfumu Saulo, Mfumu Saulo adabereka Yonatani, Malikisuwa, Abinadabu, ndi Esibaala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Nere anabala Kisi, ndi Kisi anabala Saulo, ndi Saulo anabala Yonatani, ndi Malikisuwa, ndi Abinadabu, ndi Esibaala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Neri anabereka Kisi. Kisi anabereka Sauli, ndipo Sauli anabereka Yonatani, Maliki-Suwa, Abinadabu ndi Esibaala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Neri anabala Kisi, ndi Kisi anabala Sauli, ndi Sauli anabala Yonatani, ndi Malikisuwa, ndi Abinadabu, ndi Esibaala.