1 Chronicles 8:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anawo anali Namani, Ahiya ndi Gera. Gerayo amene anali bambo wake wa Uza ndi Ahihudi, ndiye adatsogolera anthu osamutsidwawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
natenga ndende Naamani, ndi Ahiya, ndi Gera, ndipo, anabala Uza, ndi Ahihudi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Naamani, Ahiya ndi Gera, amene anawasamutsa ndipo anabereka Uza ndi Ahihudi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
natenga ndende Namani, ndi Ahiya, ndi Gera, ndipo, anabala Uza, ndi Ahihudi.