1 Chronicles 8:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa mkazi wake Hodesi adabelekamo ana aŵa: Yobabu, Zibiya, Mesa, Malikamu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hodesi mkazi wake anambalira Yobabu, ndi Zibiya, ndi Mesa, ndi Malikamu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa mkazi wake Hodesi anabereka Yobabu, Zibiya, Mesa, Malikamu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hodesi mkazi wace anambalira Yohabu, ndi Zibiya, ndi Mesa, ndi Malikamu,