1 Chronicles 9:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panalinso Bakibakara, Heresi, Galali kudzanso Mataniya, mwana wa Mika, mwana wa Zikiri, mwana wa Asafu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Bakibakara, Heresi, ndi Galali, ndi Mataniya mwana wa Mika, mwana wa Zikiri, mwana wa Asafu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bakibakara, Heresi, Galali ndi Mataniya mwana wa Mika, mwana wa Zikiri, mwana wa Asafu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Bakabakara, Heresi, ndi Galala, ndi Mataniya mwana wa Mika, mwana wa Zikiri, mwana wa Asafu;