1 Chronicles 9:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panalinso Obadiya, mwana wa Semaya, mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni, ndiponso Berekiya, mwana wa Asa, mwana wa Elikana, amene ankakhala ku midzi yoyandikana ndi tauni ya Anetofati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Obadiya mwana wa Semaya, mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni, ndi Berekiya mwana wa Asa, mwana wa Elikana, wokhala m'midzi ya Anetofa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Obadiya mwana wa Semaya mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni ndi Berekiya mwana wa Asa, mwana wa Elikana, amene ankakhala ku midzi ya Anetofati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Obadiya mwana wa Semaya, mwana wa Galala, mwana wa Yedutuni, ndi Berekiya mwana wa Asa, mwana wa Elikana, wokhala m'midzi ya Anetofati.