1 Chronicles 9:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Aisraele oyamba kukakhala m'maiko mwao ndi m'mizinda yao anali anthu wamba, ansembe, Alevi ndi atumiki a ku Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Okhala m'dziko oyamba tsono, akukhala mwaomwao m'midzi mwao, ndiwo Israele, ansembe, Alevi, ndi Anetini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anthu oyamba kukhala mʼmadera awo anali Aisraeli wamba, ansembe, Alevi ndi otumikira ku Nyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Okhala m'dziko oyamba tsono, akukhala mwao mwao m'roidzi mwao, ndiwo Israyeli, ansembe, Alevi, ndi Anetini.