1 Chronicles 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Finehasi, mwana wa Eleazara ndiye ankaŵalamulira kale. Chauta anali naye!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Finehasi mwana wa Eleazara anali mtsogoleri wao kale, ndipo Yehova anali naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Masiku oyamba Finehasi mwana wa Eliezara anali woyangʼanira alonda apakhomo ndipo Yehova anali naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi a Pinehasi mwana wa Eleazara anali mtsogoleri wao kale, ndipo Yehova anali naye.