1 Chronicles 9:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zekariya mwana wa Meselemiya ankadikira pa khomo la chipata cha chihema chamsonkhano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zekariya mwana wa Meselemiya anali wodikira pakhomo pa chihema chokomanako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zekariya mwana wa Meselemiya anali mlonda woyangʼanira pa chipata cha tenti ya msonkhano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zekariya mwana wa Meselemiya anali wodikira pakhomo pa cihema cokomanako.