1 Chronicles 9:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero iwowo ndi zidzukulu zao ankayang'anira ndi kumalonda pa makomo a Nyumba ya Chauta, monga ankachitira ku chihema chija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo iwo ndi ana ao anayang'anira zipata za kunyumba ya Yehova, ndiyo nyumba ya Kachisi, m'udikiro wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ndi zidzukulu zawo anali oyangʼanira zipata za nyumba ya Yehova imene imatchedwa Tenti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo iwo ndi ana ao anayang'anira zipata za ku nyumba ya Yehova, ndiyo nyumba ya kacisi, m'udikiro wao.