1 Chronicles 9:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alondawo anali ku mbali zonse zinai, kuvuma, kuzambwe, kumpoto ndi kumwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa mbali zinai panali odikira kum'mawa, kumadzulo, kumpoto, ndi kumwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alonda apakhomowa anali mbali zonse zinayi: kummawa, kumadzulo, kumpoto ndi kummwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa mbali zinai panali odikira kum'mawa, kumadzulo, kumpoto, ndi kumwela.