1 Chronicles 9:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usiku ankakhala mozungulira Nyumba ya Chauta, pakuti iwowo ndiwo amene adaasenza udindo waulonda, ndipo anali ndi ntchito yotsekula Nyumbayo m'maŵa mulimonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amagona usiku m'zipinda zozinga nyumba ya Mulungu, popeza udikiro wake ndi wao; kuitsegula m'mawa ndi m'mawa ndi kwaonso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amakhala usiku wonse atayima mozungulira Nyumba ya Mulungu, chifukwa anayenera kuyilondera. Ndipo anali ndi kiyi wotsekulira mmawa uliwonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amagona usiku m'zipinda zozinga nyumba ya Mulungu, popeza udikiro wace ndi wao; kuitsegula m'mawa ndi m'mawa ndi kwaonso.