1 Chronicles 9:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo Matitiya, mmodzi mwa Alevi, mwana wachisamba wa Salumu Mkora, ankayang'anira kaphikidwe ka makeke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Matitiya wina wa Alevi, ndiye mwana woyamba wa Salumu Mkora, anaikidwa ayang'anire zokazingidwa m'ziwaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mlevi wotchedwa Matitiya mwana woyamba wa Salumu wa mʼbanja la Kora, anapatsidwa udindo woyangʼanira zophikidwa mʼziwaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Matitiya wina wa Alevi, ndiye mwana woyamba wa Salumu Mkora, anaikidwa ayang'anire zokazingidwa m'ziwaya.