1 Chronicles 9:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yeiyele amene adaamanga mzinda wa Gibiyoni, ankakhala ku Gibiyoni komweko. Mkazi wake anali Maaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'Gibiyoni munakhala atate wa Gibiyoni Yeiyele, dzina la mkazi wake ndiye Maaka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeiyeli abambo a Gibiyoni ankakhala ku Gibiyoni. Dzina la akazi awo linali Maaka,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'Gibeoni munakhala atate wa Gibeoni Yeieli, dzina la mkazi wace ndiye Maaka;