1 Chronicles 9:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wake wachisamba anali Abidoni ndipo pambuyo pa iyeyo panali Zuri, Kisi, Baala, Nere, Nadabu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mwana wake woyamba ndiye Abidoni, opondana naye ndi Zuri, ndi Kisi, ndi Baala, ndi Nere, ndi Nadabu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo mwana wawo woyamba kubadwa anali Abidoni, motsatana ndi Zuri, Kisi, Baala, Neri, Nadabu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mwana wace woyamba ndiye Abidoni, opandana naye ndi Zuri, ndi Kisi, ndi Baala, ndi Neri, ndi Nadabu,