1 Chronicles 9:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Moza adabereka Bineya, Bineya adabereka Rafaya, Rafaya adabereka Eleasa, Eleasa adabereka Azele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Moza anabala Bineya, ndi Refaya mwana wake, Eleasa mwana wake, Azele mwana wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moza anabereka Bineya. Ana ake anali Refaya, Eleasa ndi Azeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Moza anabala Bineya, ndi Refaya mwana wace, Eleasa mwana wace; Azeli mwana wace;