1 Chronicles 9:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Azele anali ndi ana asanu ndi mmodzi ndipo maina ao naŵa: Azirikamu, Bokeru, Ismaele, Seyariya, Obadiya ndi Hanani. Onseŵa anali ana a Azele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Azele anali nao ana asanu ndi mmodzi, maina ao ndi awa; Azirikamu, Bokeru, ndi Ismaele, ndi Seyariya, ndi Obadiya, ndi Hanani; awa ndi ana a Azele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Azeli anali ndi ana asanu ndi mmodzi ndipo mayina awo anali awa: Azirikamu, Bokeru, Ismaeli, Seariya, Obadiya ndi Hanani. Awa anali ana a Azeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Azeli anali nao ana asanu ndi mmodzi, maina ao ndi awa; Azrikamu, Bokeru, ndi Ismayeli, ndi Seariya, ndi Obadiya, ndi Hanani; awa ndi ana a Azeli.