1 Chronicles 9:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A kwa Abenjamini anali aŵa: Salu, mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuwa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a ana a Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
A fuko la Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuya;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a ana a Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodavia, mwana wa Hasenuwa;