1 Chronicles 9:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ibineya mwana wa Yerohamu, Ela mwana wa Uzi, mwana wa Mikiri ndiponso Mesulamu, mwana wa Sefatiya, mwana wa Reuwele, mwana wa Ibineya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Ibineya mwana wa Yerohamu, ndi Ela mwana wa Uzi, mwana wa Mikiri, ndi Mesulamu mwana wa Sefatiya, mwana wa Reuwele, mwana wa Ibineya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ibineya mwana wa Yerohamu; Ela mwana wa Uzi, mwana wa Mikiri; ndi Mesulamu mwana wa Sefatiya, mwana wa Reueli mwana wa Ibiniya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Ibineya mwana wa Yerohamu, ndi Ela mwana wa Uzi, mwana-wa Mikiri, ndi Mesulamu mwana wa Sefatiya, mwana wa Reueli, mwana wa Ibniya,