1 Corinthians 1:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ena a m'banja la Koloe andifotokozera kuti pali kukangana pakati panu, abale anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti zinamveka kwa ine za inu, abale anga, ndi iwo a kwa Koloe, kuti pali makani pakati pa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale anga, ena a ku nyumba ya Kloe andidziwitsa kuti pali mkangano pakati panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti zinamveka kwa ine za inu, abale anga, ndi iwo a kwa Kloe, kuti pali makani pakati pa inu.