1 Corinthians 1:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimene ndikufuna kunena nchakuti aliyense mwa inu akungonena zakezake. Wina akuti, “Ine ndine wa Paulo,” winanso akuti, “Ine ndine wa Apolo,” wina akuti, “Ine ndine wa Kefa,” winanso akuti, “Ine ndine wa Khristu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ichi ndinena, kuti yense wa inu anena, Ine ndine wa Paulo; koma ine wa Apolo; koma ine wa Kefa; koma ine wa Khristu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimene ndikutanthauza ndi ichi: wina amati, “Ndimatsatira Paulo,” wina, “Ndimatsatira Apolo,” wina, “Ndimatsatira Kefa,” winanso, “Ndimatsatira Khristu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ici ndinena, kuti yense wa inu anena, Ine ndine wa Paulo; koma ine wa Apolo; koma ine wa Kefa; koma ine wa Kristu.