1 Corinthians 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimayamika Mulungu kuti pakati panupo sindidabatize wina aliyense, kupatula Krispo ndi Gayo basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiyamika Mulungu kuti sindinabatiza mmodzi yense wa inu, koma Krispo ndi Gayo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikuyamika kuti sindinabatizepo mmodzi mwa inu kupatula Krispo ndi Gayo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiyamika Mulungu kuti sindinabatiza mmodzi yense wa inu, koma Krisipo ndi Gayo;