1 Corinthians 1:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inde ndidabatizanso Stefanasi ndi a m'banja mwake, koma sindikumbukira kuti pali winanso amene ndidamubatiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndinabatizanso a pa banja la Stefanasi; za ena, sindidziwa ngati ndinabatiza wina yense.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Inde, ine ndinabatizanso a mʼbanja la Stefano, koma sindikumbukira ngati ndinabatizanso wina aliyense).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndinabatizanso a pa banja la Stefana; za ena, sindidziwa ngati ndinabatiza wina yense.