1 Corinthians 1:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti, “Ndidzaononga nzeru za anthu anzeru, ndidzathetsa kuchenjera kwa anthu ochenjera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti kulembedwa, Ndidzaononga nzeru za anzeru, ndi kuchenjera kwa ochenjera ndidzakutha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti kwalembedwa kuti, “Ine ndidzawononga nzeru za anthu anzeru; luntha la anthu aluntha Ine ndidzalinyoza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti kulembedwa, Ndidzaononga nzeru za anzeru, Ndi kucenjerakwa ocenjera odidzakutha.