1 Corinthians 1:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake, monga Malembo anenera, “Wofuna kunyada, anyadire Ambuye.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti monga mwalembedwa, Iye amene adzitamanda, adzitamande mwa Ambuye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho poti zinalembedwa kuti, “Ngati munthu akufuna kunyadira, anyadire mwa Ambuye.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti monga mwalembedwa, iye amene adzitamanda, adzitamande mwa Ambuye.