1 Corinthians 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi mwa Khristu mwakhala anthu olemera pa zonse, makamaka pa kulankhula ndi pa kudziŵa zinthu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti m'zonse munalemezedwa mwa Iye, m'mau onse, ndi chidziwitso chonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mwa Iye mwalemekezedwa mʼnjira iliyonse, mʼkuyankhula kwanu konse ndi mʼkudziwa kwanu konse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti m'zonse muoalemezedwa mwa iye, m'mau onse, ndi cidziwitso conse;