1 Corinthians 10:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono amene akuganiza kuti waimirira molimba, achenjere kuti angagwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake iye wakuyesa kuti ali chilili, ayang'anire kuti angagwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho, ngati mukuganiza kuti mwayima mwamphamvu, samalani mungagwe!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace iyewakuyesa kuti ali ciriri, ayang'anire kuti angagwe,