1 Corinthians 10:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikulankhula nanu ngati anthu anzeru. Muweruze nokha zimene ndikunenazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinena monga kwa anzeru; lingirirani inu chimene ndinena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikuyankhula kwa a anthu anzeru zawo, nokha muweruze pa zimene ndikunenazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinena monga kwa anzeru; lingirirani inu cimene ndinena.