1 Corinthians 10:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti, “Dziko lapansi ndi zonse zam'menemo ndi za Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti dziko lapansi lili la Ambuye, ndi kudzala kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza kuti, “Dziko lapansi ndi la Ambuye ndi zonse za mʼmenemo ndi zake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti dziko lapansi liri la Ambuye, ndi kudzala kwace.