1 Corinthians 10:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ine ndikuthokoza Mulungu chifukwa cha chakudya changa, nanga munthu angandinyoze bwanji chifukwa cha chakudya chimene ndikuchilandira mothokoza Mulungu?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ine ndilandirako mwachisomo, ndinenezedwa bwanji chifukwa cha ichi chimene ndiyamikapo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ndikuyamika Mulungu chifukwa cha chakudya, nanga munthu angandinyoze bwanji pa zinthu zomwe ndayamikira nazo Mulungu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ine ndilandirako mwacisomo, ndinenezedwa bwanji cifukwa ca ici cimene ndiyamikapo?