1 Corinthians 10:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe ambirimbiri mwa iwo Mulungu sadakondwere nawo, kotero kuti adafera m'chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ochuluka a iwo Mulungu sanakondwera nao; pakuti anamwazika m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale zinali choncho, Mulungu sanakondwere ndi ambiri a iwo, motero ambiri mwa iwo anafera mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ocuruka a iwo Mulungu sanakondwera nao; pakuti anamwazika m'cipululu.