1 Corinthians 11:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono, chifukwa cha angelo, mkazi azivala kanthu kumutu, kuti chikhale chizindikiro cha ulemu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma mkazi chifukwa cha mwamuna; chifukwa cha ichi mkazi ayenera kukhala nao ulamuliro pamutu pake, chifukwa cha angelo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chifukwa ichi, ndiponso pa chifukwa cha angelo, mkazi akuyenera kukhala ndi chizindikiro cha ulamuliro wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma mkazi cifukwa ca mwamuna; cifukwa ca ici mkazi ayenera kukhala nao ulamuliro pamutu pace, cifukwa ca angelo.