1 Corinthians 11:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumati mukamadya, aliyense angoyambapo kudya chakudya chakechake, kotero kuti wina amakhala ndi njala, m'menemo wina waledzera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti pakudyaku yense athanga watenga mgonero wake wa yekha, ndipo wina ali ndi njala, ndi wina aledzera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mukamadya, aliyense amangodzidyera zomwe anakonza. Wina amakhala ndi njala pamene wina amaledzera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti pakudyaku yense athanga watenga mgonero wace wa yekha, ndipo wina ali ndi njala, ndi wina aledzera.