1 Corinthians 11:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono abale anga, pamene musonkhana kuti mudye Mgonero wa Ambuye, muzidikirana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake, abale anga, posonkhanira kudya, lindanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiye tsono abale anga, pamene musonkhana pa chakudya, mudikirirane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace, abale anga, posonkhanira kudya, lindanani.