1 Corinthians 11:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati mwamuna apemphera kapena kulalika mau a Mulungu, atavala kanthu kumutu, akunyoza mutu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwamuna yense woveka mutu, popemphera kapena ponenera, anyoza mutu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwamuna aliyense wopemphera kapena kunenera ataphimba mutu wake akunyoza mutu wakewo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwamuna yense wobveka mutu, popemphera kapena ponenera, anyoza mutu wace.