1 Corinthians 11:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu mwamuna sadapangidwe kuchokera kwa mkazi, koma mkazi ndiye adapangidwa kuchokera kwa mwamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwamuna sakhala wa kwa mkazi; koma mkazi wa kwa mwamuna;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mwamuna sachokera kwa mkazi, koma mkazi kwa mwamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwamuna sakhala wa kwa mkazi; koma mkazi wa kwa mwamuna;