1 Corinthians 11:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiponso mwamuna sadalengedwe chifukwa cha mkazi, koma mkazi ndiye adalengedwa chifukwa cha mwamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakutinso mwamuna sanalengedwa chifukwa cha mkazi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mwamuna sanalengedwe chifukwa cha mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakutinso mwamuna sanalengedwa cifukwa ca mkazi;