1 Corinthians 12:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amachititsa anthu zonsezi ndi Mzimu Woyera mmodzi yemweyo. Amagaŵira munthu aliyense monga momwe Iye afuna kumgaŵira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma zonse izi achita Mzimu mmodzi yemweyo, nagawira yense pa yekha monga afuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zonsezi ndi ntchito za Mzimu mmodzi yemweyo, ndipo amapereka kwa munthu aliyense monga momwe Mzimuyo wafunira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma zonse izi acita Mzimu mmodzi yemweyo, nagawira yense payekha monga afuna.