1 Corinthians 12:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thupitu si chiwalo chimodzi chokha ai, koma lili ndi ziwalo zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutinso thupi silikhala chiwalo chimodzi, koma zambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano thupi silinapangidwe ndi chiwalo chimodzi koma ndi ziwalo zambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakutinso thupisilikhala ciwalo cimodzi, koma zambiri.