1 Corinthians 12:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ziwalo zonse zikadangokhala chiwalo chimodzi, sipakadakhala thupi konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati zonse zikadakhala chiwalo chimodzi, likadakhala kuti thupi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nanga zonse zikanakhala chiwalo chimodzi, ndiye thupi likanakhala lotani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati zonse zikadakhala ciwalo cimodzi, likadakhala kuti thupi?