1 Corinthians 12:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komatu ziwalo nzambiri, ngakhale thupi ndi limodzi lokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsopano pali ziwalo zambiri, koma thupi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmene zililimu, pali ziwalo zambiri koma thupi ndi limodzi lokha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kama tsopano pali ziwalo zambiri, kama thupi limodzi.