1 Corinthians 12:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero diso silingauze dzanja kuti, “Ndilibe nawe ntchito.” Ndiponso mutu sungauze mapazi kuti, “Ndilibe nanu ntchito.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo diso silingathe kunena kwa dzanja, Sindikufuna iwe, kapenanso mutu kwa mapazi, Sindikufunani inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Diso silingawuze dzanja kuti, “Iwe sindikukufuna!” Ndipo mutu sungawuze phazi kuti “Iwe sindikukufuna!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo dise silingathe kunena kwa dzanja, Sindikufuna iwe, kapenanso mutu kwa mapazi, Sindikufunani inu.