1 Corinthians 12:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwenikwenitu ziwalo zimene zimaoneka ngati zofooka, ndizo zofunika kopambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma makamakatu ziwalozo zoyesedwa zofooka m'thupi, zifunika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmalo mwake, ziwalo zathupi zimene zimaoneka ngati zofowoka ndizo zili zofunikira kwambiri,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma makamakatu ziwalozo zoyesedwa zofoka m'thupi, zifunika;