1 Corinthians 12:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adachita zimenezi kuti pasakhale kugaŵikana m'thupi, koma kuti ziwalo zonse zizisamalirana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti kusakhale chisiyano m'thupi; koma kuti ziwalo zifanane ndi kusamalana china ndi chinzake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti pasakhale kugawikana mʼthupi koma kuti ziwalo zonse zisamalirane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma kuti ziwalo zifanane ndi kusamalana cinandicinzace,